Surgery

Ku Chipatala cha Blessings ku Lumbadzi kubwera madokotala ndi ma nurse ochokera ku America kudzachita ma operation pa 4 June 2017 kwa sabata imodzi. Dokotala m’modzi wa azibambo adzachita ma operation a (hernia), kuchotsa zotupa ndi zina. Dokotala wina wa amai adzapanga ma operation ochotsa zotupa mmimba. A clinical officer adzaonana ndi wodwala asanaonane ndi ma dokotala. Padzakhala kulipira mtengo wa K500 (consultation) kuti awonane ndi a clinic officer. Fulumirani mubwere nsanga kudzalembetsa kuti mudzapeze malo. Imbani phone ku 0999394327 (ndi WhatsApp) kuti mudziwe zambiri, kapena tumizani email ku info@blessingshospital.com. Timapezeka pa M1 ku m’poto kwa turnoff yayikulu ya Kamuzu International airport ku Lumbadzi. Timalandira ma membala a MASM, Metropolitan Health, Tobacco Control Commission, LIHACO, Malawi catering service Limited ndi Carslberg.

Blessings Hospital would like to inform the general public that doctors and nurses from the United States of America will be performing operations at Blessings Hospital the week of 4 June 2017.  Men and women who may have a mass or growth, such as a hernia, should come for screening.  A doctor will also be doing special operations on women.  Patients must first be screened by a clinical officer.  The cost to see the clinical officer is K500 for consultation.  Make your appointment and come soon to be put on the list.  Call 0999394327  (and on WhatsApp) with questions or to make an appointment.  You can also email us at info@blessingshospital.com.   We are located on M1 just past the airport turnoff in Lumbadzi.  We accept MASM, Metropolitan Health, Tobacco Control Commission, LIHACO, Malawi catering service Limited, and Carslberg.

DSC04580